Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 11:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Zitatero, Davide anatuma nthumwi kukafufuza za mkaziyo.+ Ndiyeno munthu wina ananena kuti: “Kodi ameneyu si Bati-seba+ mwana wa Eliyamu,*+ mkazi wa Uriya+ Mhiti?”+

  • 2 Samueli 11:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Nyengo yolira maliro+ itatha, nthawi yomweyo Davide anatumiza nthumwi kukatenga Bati-seba ndi kubwera naye kunyumba kwake, ndipo anakhala mkazi wake.+ Patapita nthawi, anamuberekera mwana wamwamuna. Koma zimene Davide anachitazi zinamuipira kwambiri Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena