Genesis 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kanani anabereka Sidoni+ mwana wake woyamba, kenako anabereka Heti.+ Genesis 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ahiti,+ Aperezi,+ Arefai,+ Deuteronomo 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 chifukwa muyenera kuwawononga ndithu. Mukawononge Ahiti, Aamori, Akanani, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi,+ monga mmene Yehova Mulungu wanu anakulamulirani.
17 chifukwa muyenera kuwawononga ndithu. Mukawononge Ahiti, Aamori, Akanani, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi,+ monga mmene Yehova Mulungu wanu anakulamulirani.