2 Samueli 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Davide anayamba kutonthoza mkazi wake Bati-seba.+ Kuwonjezera apo, analowa kwa iye ndipo anagona naye. Patapita nthawi, anamuberekera mwana wamwamuna+ amene anamutcha dzina lakuti Solomo.*+ Yehova anam’konda mwana ameneyu.+ 1 Mafumu 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Natani+ anauza Bati-seba+ mayi wake wa Solomo+ kuti: “Kodi simunamve kuti Adoniya mwana wa Hagiti+ wakhala mfumu koma mbuye wathu Davide sakuzidziwa n’komwe zimenezi?
24 Ndiyeno Davide anayamba kutonthoza mkazi wake Bati-seba.+ Kuwonjezera apo, analowa kwa iye ndipo anagona naye. Patapita nthawi, anamuberekera mwana wamwamuna+ amene anamutcha dzina lakuti Solomo.*+ Yehova anam’konda mwana ameneyu.+
11 Kenako Natani+ anauza Bati-seba+ mayi wake wa Solomo+ kuti: “Kodi simunamve kuti Adoniya mwana wa Hagiti+ wakhala mfumu koma mbuye wathu Davide sakuzidziwa n’komwe zimenezi?