2 Samueli 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zitatero, Davide anatuma nthumwi kukafufuza za mkaziyo.+ Ndiyeno munthu wina ananena kuti: “Kodi ameneyu si Bati-seba+ mwana wa Eliyamu,*+ mkazi wa Uriya+ Mhiti?”+ 2 Samueli 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 N’chifukwa chiyani unanyoza mawu a Yehova mwa kuchita chinthu choipa+ pamaso pake? Uriya Mhiti unamupha ndi lupanga, ndipo mkazi wake unamutenga kukhala mkazi wako,+ pamene Uriyayo unamupha ndi lupanga+ la ana a Amoni.
3 Zitatero, Davide anatuma nthumwi kukafufuza za mkaziyo.+ Ndiyeno munthu wina ananena kuti: “Kodi ameneyu si Bati-seba+ mwana wa Eliyamu,*+ mkazi wa Uriya+ Mhiti?”+
9 N’chifukwa chiyani unanyoza mawu a Yehova mwa kuchita chinthu choipa+ pamaso pake? Uriya Mhiti unamupha ndi lupanga, ndipo mkazi wake unamutenga kukhala mkazi wako,+ pamene Uriyayo unamupha ndi lupanga+ la ana a Amoni.