2 Samueli 23:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 ndi Uriya+ Mhiti, onse pamodzi 37. 1 Mafumu 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anatero popeza Davide anachita zoyenera pamaso pa Yehova, ndipo sanapatuke pa chilichonse chimene Mulungu anamulamula masiku onse a moyo wake,+ kupatulapo pa nkhani ya Uriya Mhiti.+ 1 Mbiri 11:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Uriya+ Mhiti,+ Zabadi mwana wa Alai,
5 Anatero popeza Davide anachita zoyenera pamaso pa Yehova, ndipo sanapatuke pa chilichonse chimene Mulungu anamulamula masiku onse a moyo wake,+ kupatulapo pa nkhani ya Uriya Mhiti.+