2 Samueli 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano usiku umenewo, Yehova analankhula+ ndi Natani, kuti: 2 Samueli 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Natani anauza Davide mawu onsewa ndiponso masomphenya onse amene anaona.+