2 Samueli 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano usiku umenewo, Yehova analankhula+ ndi Natani, kuti: 1 Mbiri 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Natani anauza Davide mawu onsewa ndi masomphenya onse amene anaona.+ 2 Petulo 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa ulosi sunayambe wanenedwapo mwa kufuna kwa munthu,+ koma anthu analankhula mawu ochokera kwa Mulungu+ motsogoleredwa ndi mzimu woyera.+
21 Chifukwa ulosi sunayambe wanenedwapo mwa kufuna kwa munthu,+ koma anthu analankhula mawu ochokera kwa Mulungu+ motsogoleredwa ndi mzimu woyera.+