2 Samueli 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Masiku ako akadzakwana,+ ndipo ukadzagona pamodzi ndi makolo ako,+ pamenepo ndidzautsa mbewu yako yobwera pambuyo pako, imene idzatuluka m’chiuno mwako. Ndipo ndidzakhazikitsadi ufumu wake.+ 1 Mbiri 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsopano mfumu Davide inauza mpingo wonse+ kuti: “Solomo mwana wanga, amene Mulungu wamusankha,+ ndi wamng’ono+ ndi wosakhwima. Koma ntchitoyi ndi yaikulu chifukwa chinyumba chachikuluchi, si cha munthu ayi,+ koma ndi cha Yehova Mulungu.
12 Masiku ako akadzakwana,+ ndipo ukadzagona pamodzi ndi makolo ako,+ pamenepo ndidzautsa mbewu yako yobwera pambuyo pako, imene idzatuluka m’chiuno mwako. Ndipo ndidzakhazikitsadi ufumu wake.+
29 Tsopano mfumu Davide inauza mpingo wonse+ kuti: “Solomo mwana wanga, amene Mulungu wamusankha,+ ndi wamng’ono+ ndi wosakhwima. Koma ntchitoyi ndi yaikulu chifukwa chinyumba chachikuluchi, si cha munthu ayi,+ koma ndi cha Yehova Mulungu.