1 Mafumu 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano Yehova Mulungu wanga, mwaika mtumiki wanune kukhala mfumu m’malo mwa Davide bambo anga. Komatu ndine mwana+ ndipo sindikudziwa zinthu zambiri.+ Miyambo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ine ndinali mwana wabwino kwa bambo anga.+ Ndinali wokondedwa kwambiri ndiponso mmodzi yekhayo pamaso pa mayi anga.+
7 Tsopano Yehova Mulungu wanga, mwaika mtumiki wanune kukhala mfumu m’malo mwa Davide bambo anga. Komatu ndine mwana+ ndipo sindikudziwa zinthu zambiri.+
3 Pakuti ine ndinali mwana wabwino kwa bambo anga.+ Ndinali wokondedwa kwambiri ndiponso mmodzi yekhayo pamaso pa mayi anga.+