1 Mafumu 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ine ndatsala pang’ono kufa,+ choncho iweyo uchite zinthu mwamphamvu+ ndipo ukhale wolimba mtima.+ 1 Mafumu 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Solomo anakhala pampando wachifumu wa Davide bambo ake,+ ndipo m’kupita kwa nthawi, ufumu wake unakhazikika.+
12 Solomo anakhala pampando wachifumu wa Davide bambo ake,+ ndipo m’kupita kwa nthawi, ufumu wake unakhazikika.+