Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 31:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Limbani mtima ndipo chitani zinthu mwamphamvu.+ Musawaope kapena kuchita nawo mantha,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pang’ono.”+

  • Yoswa 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu,+ pakuti ndiwe amene utsogolere anthuwa kuti akalandire dziko+ limene ndinalumbirira makolo awo kuti ndidzawapatsa.+

  • 1 Mbiri 28:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kenako Davide anauza Solomo mwana wake kuti: “Limba mtima,+ ugwire ntchitoyi mwamphamvu. Usaope+ kapena kuchita mantha+ chifukwa Yehova Mulungu, Mulungu wanga, ali ndi iwe.+ Sadzakutaya+ kapena kukusiya, kufikira ntchito yonse yokhudza utumiki wa nyumba ya Yehova itatha.

  • Aefeso 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Potsiriza ndikuti, pitirizani kupeza mphamvu+ kuchokera kwa Ambuye ndiponso kuchokera ku mphamvu+ zake zazikulu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena