Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 1:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Yoswa mwana wa Nuni, amene akukutumikira ndi amene akalowamo.’+ Mulungu wamulimbitsa+ chifukwa ndi amene adzatsogolere ana a Isiraeli pokalandira dzikolo.)

  • Deuteronomo 31:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndiyeno Mulungu anaika Yoswa mwana wa Nuni+ kukhala mtsogoleri, ndipo anamuuza kuti: “Limba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu,+ chifukwa iwe ndi amene udzalowetsa ana a Isiraeli m’dziko limene ndawalumbirira,+ ndipo ine ndidzapitiriza kukhala nawe.”

  • Salimo 27:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yembekezera Yehova.+ Limba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu.+

      Yembekezera Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena