Yoswa 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu,+ pakuti ndiwe amene utsogolere anthuwa kuti akalandire dziko+ limene ndinalumbirira makolo awo kuti ndidzawapatsa.+ Salimo 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yembekezera Yehova.+ Limba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu.+Yembekezera Yehova.+ Salimo 118:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova ali kumbali yanga, sindidzaopa.+Munthu wochokera kufumbi angandichite chiyani?+
6 Ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu,+ pakuti ndiwe amene utsogolere anthuwa kuti akalandire dziko+ limene ndinalumbirira makolo awo kuti ndidzawapatsa.+