Salimo 31:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Limbani mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu,+Inu nonse amene mukuyembekezera Yehova.+ Yesaya 40:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 koma anthu odalira+ Yehova adzapezanso mphamvu.+ Iwo adzaulukira m’mwamba ngati ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka. Adzayenda koma osatopa.”+
31 koma anthu odalira+ Yehova adzapezanso mphamvu.+ Iwo adzaulukira m’mwamba ngati ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka. Adzayenda koma osatopa.”+