Ekisodo 33:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Yehova anali kulankhula ndi Mose pamasom’pamaso,+ mmene munthu amalankhulira ndi munthu mnzake. Mose akabwerera kumsasa, mtumiki wake+ Yoswa, mwana wa Nuni,+ sanali kuchoka m’chihemacho, popeza anali kalinde. Numeri 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo, Yoswa mwana wa Nuni, yemwe anali mtumiki+ wa Mose kuyambira ali mnyamata, anayankhira kuti: “Mbuyanga Mose, kawaletseni amenewo!”+ Numeri 14:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma mwa amuna amene anakazonda dzikolo, Yoswa mwana wa Nuni ndi Kalebe mwana wa Yefune, adzakhalabe ndi moyo ndithu.”’”+
11 Pamenepo Yehova anali kulankhula ndi Mose pamasom’pamaso,+ mmene munthu amalankhulira ndi munthu mnzake. Mose akabwerera kumsasa, mtumiki wake+ Yoswa, mwana wa Nuni,+ sanali kuchoka m’chihemacho, popeza anali kalinde.
28 Pamenepo, Yoswa mwana wa Nuni, yemwe anali mtumiki+ wa Mose kuyambira ali mnyamata, anayankhira kuti: “Mbuyanga Mose, kawaletseni amenewo!”+
38 Koma mwa amuna amene anakazonda dzikolo, Yoswa mwana wa Nuni ndi Kalebe mwana wa Yefune, adzakhalabe ndi moyo ndithu.”’”+