Numeri 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo, Yoswa mwana wa Nuni, yemwe anali mtumiki+ wa Mose kuyambira ali mnyamata, anayankhira kuti: “Mbuyanga Mose, kawaletseni amenewo!”+ Deuteronomo 1:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Yoswa mwana wa Nuni, amene akukutumikira ndi amene akalowamo.’+ Mulungu wamulimbitsa+ chifukwa ndi amene adzatsogolere ana a Isiraeli pokalandira dzikolo.) Yoswa 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Mose mtumiki wa Yehova atamwalira, Yehova analankhula ndi Yoswa+ mwana wa Nuni, mtumiki+ wa Mose, kuti:
28 Pamenepo, Yoswa mwana wa Nuni, yemwe anali mtumiki+ wa Mose kuyambira ali mnyamata, anayankhira kuti: “Mbuyanga Mose, kawaletseni amenewo!”+
38 Yoswa mwana wa Nuni, amene akukutumikira ndi amene akalowamo.’+ Mulungu wamulimbitsa+ chifukwa ndi amene adzatsogolere ana a Isiraeli pokalandira dzikolo.)
1 Mose mtumiki wa Yehova atamwalira, Yehova analankhula ndi Yoswa+ mwana wa Nuni, mtumiki+ wa Mose, kuti: