Ekisodo 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Mose ndi Yoswa mtumiki wake ananyamuka, ndipo Mose anakwera m’phiri la Mulungu woona.+ Numeri 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo, Yoswa mwana wa Nuni, yemwe anali mtumiki+ wa Mose kuyambira ali mnyamata, anayankhira kuti: “Mbuyanga Mose, kawaletseni amenewo!”+
28 Pamenepo, Yoswa mwana wa Nuni, yemwe anali mtumiki+ wa Mose kuyambira ali mnyamata, anayankhira kuti: “Mbuyanga Mose, kawaletseni amenewo!”+