Deuteronomo 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Taona, nthawi ya kufa kwako yayandikira.+ Itana Yoswa, ndipo muime m’chihema chokumanako kuti ndimuike kukhala mtsogoleri.”+ Choncho Mose ndi Yoswa anapita ndi kukaima m’chihema chokumanako.+
14 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Taona, nthawi ya kufa kwako yayandikira.+ Itana Yoswa, ndipo muime m’chihema chokumanako kuti ndimuike kukhala mtsogoleri.”+ Choncho Mose ndi Yoswa anapita ndi kukaima m’chihema chokumanako.+