Numeri 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chongofunika n’chakuti musam’pandukire Yehova.+ Komanso anthu a m’dzikolo musawaope,+ chifukwa ali ngati chakudya kwa ife. Alibenso chitetezo,+ koma ifeyo Yehova ali nafe.+ Musawaope ayi.”+ Deuteronomo 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Ndiye ine ndinakuuzani kuti, ‘Musachite mantha kapena kuwaopa.+ Deuteronomo 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Usaiope.+ Nthawi zonse uzikumbukira zimene Yehova Mulungu wako anachitira Farao ndi Iguputo yense.+ Salimo 56:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine ndidzadalira inu, tsiku lililonse limene ndingachite mantha.+
9 Chongofunika n’chakuti musam’pandukire Yehova.+ Komanso anthu a m’dzikolo musawaope,+ chifukwa ali ngati chakudya kwa ife. Alibenso chitetezo,+ koma ifeyo Yehova ali nafe.+ Musawaope ayi.”+
18 Usaiope.+ Nthawi zonse uzikumbukira zimene Yehova Mulungu wako anachitira Farao ndi Iguputo yense.+