Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 14:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Chilimikani ndi kuona chipulumutso cha Yehova chimene akuchitireni lero.+ Pakuti Aiguputo amene mukuwaona lerowa simudzawaonanso, ndithu, simudzawaonanso.+

  • Salimo 105:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Iwowa anasonyeza Aiguputo zizindikiro za Mulungu,+

      Ndi zozizwitsa m’dziko la Hamu.+

  • Salimo 135:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Wochita zimenezi ndiye anapha ana oyamba kubadwa a ku Iguputo,+

      Anapha ana a anthu ngakhalenso ana a nyama.+

  • Machitidwe 13:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mulungu wa anthu awa Aisiraeli, anasankha makolo athu akale. Anakweza anthu amenewa pamene anali kukhala m’dziko lachilendo la Iguputo, ndipo anawatulutsa mmenemo ndi dzanja lokwezeka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena