Ekisodo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Choncho uwauze ana a Isiraeli kuti, ‘Ine ndine Yehova. Ndithu, ndidzakutulutsani mu Iguputo ndi kukuchotserani goli lawo, ndipo ndidzakulanditsani ku ukapolo wawo.+ Ndidzakuwombolani ndi dzanja langa lotambasula komanso ndi ziweruzo zamphamvu.+ Ekisodo 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Yehova analola Farao mfumu ya Iguputo kuumitsa mtima wake,+ ndipo anathamangira ana a Isiraeli pamene iwo anali kutuluka ndi dzanja lokwezeka.*+ Deuteronomo 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu.+ Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, mwa anthu onse okhala padziko lapansi.+
6 “Choncho uwauze ana a Isiraeli kuti, ‘Ine ndine Yehova. Ndithu, ndidzakutulutsani mu Iguputo ndi kukuchotserani goli lawo, ndipo ndidzakulanditsani ku ukapolo wawo.+ Ndidzakuwombolani ndi dzanja langa lotambasula komanso ndi ziweruzo zamphamvu.+
8 Choncho Yehova analola Farao mfumu ya Iguputo kuumitsa mtima wake,+ ndipo anathamangira ana a Isiraeli pamene iwo anali kutuluka ndi dzanja lokwezeka.*+
6 Pakuti ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu.+ Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, mwa anthu onse okhala padziko lapansi.+