Numeri 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ananyamuka ku Ramese+ m’mwezi woyamba,+ pa tsiku la 15. Pasika anali atachitika dzulo lake,+ pamene ana a Isiraeli ananyamuka molimba mtima* pamaso pa Aiguputo onse.+
3 Ananyamuka ku Ramese+ m’mwezi woyamba,+ pa tsiku la 15. Pasika anali atachitika dzulo lake,+ pamene ana a Isiraeli ananyamuka molimba mtima* pamaso pa Aiguputo onse.+