Genesis 47:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chotero Yosefe anakhazika bambo ake ndi abale akewo ku Iguputo. Anawapatsa malo abwino koposa a dzikolo ku Ramese,+ monga mmene Farao analamulira. Ekisodo 12:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pamenepo ana a Isiraeli ananyamuka ku Ramese+ kupita ku Sukoti.+ Amuna amphamvu oyenda pansi analipo pafupifupi 600,000, osawerengera ana.+
11 Chotero Yosefe anakhazika bambo ake ndi abale akewo ku Iguputo. Anawapatsa malo abwino koposa a dzikolo ku Ramese,+ monga mmene Farao analamulira.
37 Pamenepo ana a Isiraeli ananyamuka ku Ramese+ kupita ku Sukoti.+ Amuna amphamvu oyenda pansi analipo pafupifupi 600,000, osawerengera ana.+