Genesis 45:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inuyo, ana anu, adzukulu anu, nkhosa ndi ng’ombe zanu, ndi zonse zimene muli nazo mudzakhale m’dziko la Goseni+ pafupi ndi ine. Ekisodo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho anawaikira akulu owayang’anira pa ntchito yawo yaukapolo, kuti aziwanyamulitsa katundu mwankhanza.+ Ndipo anamangira Farao mizinda ya Pitomu ndi Ramese+ kuti ikhale mosungiramo zinthu.* Ekisodo 12:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pamenepo ana a Isiraeli ananyamuka ku Ramese+ kupita ku Sukoti.+ Amuna amphamvu oyenda pansi analipo pafupifupi 600,000, osawerengera ana.+ Numeri 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ananyamuka ku Ramese+ m’mwezi woyamba,+ pa tsiku la 15. Pasika anali atachitika dzulo lake,+ pamene ana a Isiraeli ananyamuka molimba mtima* pamaso pa Aiguputo onse.+
10 Inuyo, ana anu, adzukulu anu, nkhosa ndi ng’ombe zanu, ndi zonse zimene muli nazo mudzakhale m’dziko la Goseni+ pafupi ndi ine.
11 Choncho anawaikira akulu owayang’anira pa ntchito yawo yaukapolo, kuti aziwanyamulitsa katundu mwankhanza.+ Ndipo anamangira Farao mizinda ya Pitomu ndi Ramese+ kuti ikhale mosungiramo zinthu.*
37 Pamenepo ana a Isiraeli ananyamuka ku Ramese+ kupita ku Sukoti.+ Amuna amphamvu oyenda pansi analipo pafupifupi 600,000, osawerengera ana.+
3 Ananyamuka ku Ramese+ m’mwezi woyamba,+ pa tsiku la 15. Pasika anali atachitika dzulo lake,+ pamene ana a Isiraeli ananyamuka molimba mtima* pamaso pa Aiguputo onse.+