Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 46:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Inu mukayankhe kuti: ‘Akapolo anufe takhala tikuweta ziweto kuyambira tili ana kufikira lero, ifeyo ndi makolo athu omwe.’+ Mukayankhe choncho kuti mukhale ku Goseni,+ chifukwa aliyense woweta nkhosa Aiguputo amanyansidwa naye.”+

  • Genesis 47:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Yosefe anafikadi kwa Farao n’kumuuza kuti:+ “Bambo anga ndi abale anga abwera kuchokera ku Kanani. Abwera ndi nkhosa zawo, ng’ombe zawo ndi zonse zimene ali nazo, ndipo afikira ku Goseni.”+

  • Ekisodo 8:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pa tsiku limenelo ndidzapatula dera la Goseni kumene kuli anthu anga, kuti kusakhale tizilombo toyamwa magazi.+ Ndidzatero kuti udziwe kuti ine ndine Yehova, ndipo ndili ndi mphamvu padziko lonse lapansi.+

  • Ekisodo 9:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Koma kudera la Goseni kokha, kumene kunali ana a Isiraeli, sikunagwe matalala.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena