Ekisodo 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ine ndidzadutsa m’dziko la Iguputo usiku umenewo+ ndi kupha mwana aliyense woyamba kubadwa m’dziko la Iguputo, mwana wa munthu kapena wa chiweto.+ Ndipo ndidzapereka ziweruzo pa milungu yonse ya mu Iguputo.+ Ine ndine Yehova.+ Salimo 78:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamapeto pake anapha ana onse oyamba kubadwa mu Iguputo,+Amene ndi chiyambi cha mphamvu zawo zobereka m’mahema a Hamu.+ Salimo 136:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yamikani amene anakantha Aiguputo mwa kupha ana awo oyamba kubadwa:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
12 Ine ndidzadutsa m’dziko la Iguputo usiku umenewo+ ndi kupha mwana aliyense woyamba kubadwa m’dziko la Iguputo, mwana wa munthu kapena wa chiweto.+ Ndipo ndidzapereka ziweruzo pa milungu yonse ya mu Iguputo.+ Ine ndine Yehova.+
51 Pamapeto pake anapha ana onse oyamba kubadwa mu Iguputo,+Amene ndi chiyambi cha mphamvu zawo zobereka m’mahema a Hamu.+
10 Yamikani amene anakantha Aiguputo mwa kupha ana awo oyamba kubadwa:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+