Ekisodo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho Mose anati: “Yehova wanena kuti, ‘Pakati pa usiku ndidzalowa mu Iguputo,+ Amosi 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ‘Padzakhala kulira mokweza m’minda yonse ya mpesa+ pakuti ine ndidzadutsa pakati panu,’+ watero Yehova.
17 ‘Padzakhala kulira mokweza m’minda yonse ya mpesa+ pakuti ine ndidzadutsa pakati panu,’+ watero Yehova.