Ekisodo 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ine ndidzadutsa m’dziko la Iguputo usiku umenewo+ ndi kupha mwana aliyense woyamba kubadwa m’dziko la Iguputo, mwana wa munthu kapena wa chiweto.+ Ndipo ndidzapereka ziweruzo pa milungu yonse ya mu Iguputo.+ Ine ndine Yehova.+ Nahumu 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova wanena kuti: “Ngakhale kuti iwo anali achikwanekwane ndiponso anali ndi mphamvu zambiri, adzadulidwa+ ndipo wina adzawaukira. Pamenepo ndidzakusautsa kufikira pamene sudzafunikiranso kusautsidwa.+
12 Ine ndidzadutsa m’dziko la Iguputo usiku umenewo+ ndi kupha mwana aliyense woyamba kubadwa m’dziko la Iguputo, mwana wa munthu kapena wa chiweto.+ Ndipo ndidzapereka ziweruzo pa milungu yonse ya mu Iguputo.+ Ine ndine Yehova.+
12 Yehova wanena kuti: “Ngakhale kuti iwo anali achikwanekwane ndiponso anali ndi mphamvu zambiri, adzadulidwa+ ndipo wina adzawaukira. Pamenepo ndidzakusautsa kufikira pamene sudzafunikiranso kusautsidwa.+