Yesaya 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kukondwera ndi kusangalala zachotsedwa m’munda wako wa zipatso, ndipo m’minda ya mpesa mulibe mfuu yachisangalalo. Mulibe aliyense amene akufuula.+ Mopondera mphesa mulibe amene akuponda vinyo.+ Ndachititsa kuti kufuula kulekeke.+ Yeremiya 48:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kusangalala ndi kukondwera zachotsedwa m’munda wa zipatso ndiponso m’dziko la Mowabu.+ Ndachititsa kuti vinyo asapezeke moponderamo mphesa.+ Palibe amene adzapondaponda mphesa akufuula mosangalala. Padzamveka kufuula koma osati kwachisangalalo.’”+ Hoseya 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Malo opunthira mbewu ndiponso oponderamo mphesa sakukupatsa chakudya,+ ndipo vinyo wotsekemera akukukhumudwitsa.+
10 Kukondwera ndi kusangalala zachotsedwa m’munda wako wa zipatso, ndipo m’minda ya mpesa mulibe mfuu yachisangalalo. Mulibe aliyense amene akufuula.+ Mopondera mphesa mulibe amene akuponda vinyo.+ Ndachititsa kuti kufuula kulekeke.+
33 Kusangalala ndi kukondwera zachotsedwa m’munda wa zipatso ndiponso m’dziko la Mowabu.+ Ndachititsa kuti vinyo asapezeke moponderamo mphesa.+ Palibe amene adzapondaponda mphesa akufuula mosangalala. Padzamveka kufuula koma osati kwachisangalalo.’”+
2 Malo opunthira mbewu ndiponso oponderamo mphesa sakukupatsa chakudya,+ ndipo vinyo wotsekemera akukukhumudwitsa.+