Yesaya 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti maekala 10*+ a munda wa mpesa adzatulutsa mtsuko*+ umodzi wokha wa vinyo, ndipo mbewu zokwana muyezo umodzi wa homeri* zidzatulutsa zokolola zokwana muyezo umodzi wokha wa efa.*+ Yesaya 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “M’tsiku limenelo, pamalo alionse pamene panali mitengo ya mpesa 1,000, yokwana ndalama zasiliva 1,000,+ padzakhala tchire la zitsamba zaminga ndi udzu.+
10 Pakuti maekala 10*+ a munda wa mpesa adzatulutsa mtsuko*+ umodzi wokha wa vinyo, ndipo mbewu zokwana muyezo umodzi wa homeri* zidzatulutsa zokolola zokwana muyezo umodzi wokha wa efa.*+
23 “M’tsiku limenelo, pamalo alionse pamene panali mitengo ya mpesa 1,000, yokwana ndalama zasiliva 1,000,+ padzakhala tchire la zitsamba zaminga ndi udzu.+