-
Yeremiya 25:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 “Ndiyeno iweyo, unenere mawu onsewa, ndipo anthuwo uwauze kuti, ‘Yehova adzabangula ngati mkango ali kumwamba,+ ndipo adzafuula ali kumalo ake oyera kumene amakhala.+ Iye adzabanguliradi malo ake okhalapo a padziko lapansi. Adzaimbira anthu onse okhala padziko lapansi nyimbo yofanana ndi imene anthu oponda mphesa amaimba.’+
-