Salimo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova ali m’kachisi wake wopatulika.+Yehova, mpando wake wachifumu uli kumwamba.+Maso ake amaona, maso ake owala amasanthula+ ana a anthu. Salimo 132:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Awa ndi malo anga okhalamo mpaka muyaya.+Ndidzakhala mmenemu, pakuti ndimafunitsitsa kukhala m’malo amenewa.+
4 Yehova ali m’kachisi wake wopatulika.+Yehova, mpando wake wachifumu uli kumwamba.+Maso ake amaona, maso ake owala amasanthula+ ana a anthu.
14 “Awa ndi malo anga okhalamo mpaka muyaya.+Ndidzakhala mmenemu, pakuti ndimafunitsitsa kukhala m’malo amenewa.+