Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 81:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Yambani kuimba nyimbo+ ndipo tengani maseche,+

      Zeze womveka mosangalatsa pamodzi ndi choimbira cha zingwe.+

  • Yeremiya 7:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Pamenepo ndidzathetsa phokoso lachikondwerero, phokoso lachisangalalo, mawu a mkwati ndi mawu a mkwatibwi+ m’mizinda ya Yuda ndi m’misewu ya Yerusalemu pakuti dzikoli lidzakhala litawonongedwa.’”+

  • Yeremiya 16:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Pakuti Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘M’masiku anu ndidzathetsa phokoso lachikondwerero, phokoso lachisangalalo, mawu a mkwati ndi mawu a mkwatibwi m’malo ano, inu mukuona.’+

  • Hoseya 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo ndidzathetsa kusangalala kwake konse.+ Ndidzathetsa zikondwerero zake,+ chikondwerero cha tsiku lokhala mwezi,+ cha sabata ndi chikondwerero china chilichonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena