Habakuku 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngakhale mkuyu usaphukire maluwa,+ mtengo wa mpesa usabale zipatso, mtengo wa maolivi ulephere kubala zipatso, munda wa m’mphepete mwa phiri usatulutse chakudya,+ nkhosa ndi ng’ombe zithemo m’khola,+
17 Ngakhale mkuyu usaphukire maluwa,+ mtengo wa mpesa usabale zipatso, mtengo wa maolivi ulephere kubala zipatso, munda wa m’mphepete mwa phiri usatulutse chakudya,+ nkhosa ndi ng’ombe zithemo m’khola,+