16 Pa nthawi imeneyo zomwe zinali kuchitika n’zakuti, munthu anali kupita pamulu umene ukanakwana miyezo 20, koma anali kupeza kuti ndi wokwana miyezo 10. Munthu anali kupita moponderamo mphesa kuti akatunge miyezo 50 ya vinyo, koma anali kupeza kuti muli wongokwana miyezo 20 yokha.+