Hagai 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwafesa mbewu zambiri koma zokolola zanu n’zochepa.+ Mukudya koma simukukhuta.+ Mukumwa koma simukukhutira.* Mukuvala zovala koma simukumva kutentha. Amene akugwira ganyu akulandirira ndalama zake m’matumba obowoka.’”+ Zekariya 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Masiku amenewo asanafike, anthu ndi ziweto sanali kulandira malipiro.+ Munthu wa pa ulendo, adani anali kumusowetsa mtendere,+ chifukwa ine ndinali kuyambanitsa anthu onse.’+
6 Mwafesa mbewu zambiri koma zokolola zanu n’zochepa.+ Mukudya koma simukukhuta.+ Mukumwa koma simukukhutira.* Mukuvala zovala koma simukumva kutentha. Amene akugwira ganyu akulandirira ndalama zake m’matumba obowoka.’”+
10 Masiku amenewo asanafike, anthu ndi ziweto sanali kulandira malipiro.+ Munthu wa pa ulendo, adani anali kumusowetsa mtendere,+ chifukwa ine ndinali kuyambanitsa anthu onse.’+