Oweruza 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’masiku a Samagara+ mwana wa Anati,M’masiku a Yaeli,+ m’njira munalibe odutsamo,Ndipo oyenda m’misewu anayamba kuyenda njira zolambalala.+ 2 Mbiri 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’masiku amenewo, anthu sankayenda mwamtendere+ chifukwa panali zisokonezo zambiri pakati pa anthu onse okhala m’madera a m’dzikoli.+
6 M’masiku a Samagara+ mwana wa Anati,M’masiku a Yaeli,+ m’njira munalibe odutsamo,Ndipo oyenda m’misewu anayamba kuyenda njira zolambalala.+
5 M’masiku amenewo, anthu sankayenda mwamtendere+ chifukwa panali zisokonezo zambiri pakati pa anthu onse okhala m’madera a m’dzikoli.+