Mlaliki 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Usalole kuti pakamwa pako pakuchimwitse,+ komanso usamanene kwa mngelo+ kuti unalakwitsa.+ Kodi Mulungu woona akwiyirenji chifukwa cha mawu ako n’kuwononga ntchito ya manja ako?+ Yakobo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mumalakalaka, koma simukhala nazo. Mumapha anthu+ ndiponso mumasirira mwansanje,+ koma simupeza kanthu. Mumakangana+ ndiponso mumachita nkhondo. Simukhala ndi kanthu chifukwa simupempha.
6 Usalole kuti pakamwa pako pakuchimwitse,+ komanso usamanene kwa mngelo+ kuti unalakwitsa.+ Kodi Mulungu woona akwiyirenji chifukwa cha mawu ako n’kuwononga ntchito ya manja ako?+
2 Mumalakalaka, koma simukhala nazo. Mumapha anthu+ ndiponso mumasirira mwansanje,+ koma simupeza kanthu. Mumakangana+ ndiponso mumachita nkhondo. Simukhala ndi kanthu chifukwa simupempha.