Oweruza 11:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Atangomuona, anayamba kung’amba zovala zake+ ndi kunena kuti: “Kalanga ine mwana wanga! Wandiweramitsa ndi chisoni ndipo ine ndikukupitikitsa. Ndatsegula pakamwa panga pamaso pa Yehova, ndipo sindingathe kubweza mawu anga.”+ Yakobo 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ngati munthu akudziona ngati wopembedza,+ koma salamulira lilime lake,+ ndipo akupitiriza kunyenga mtima wake,+ kupembedza kwa munthu ameneyu n’kopanda pake.+
35 Atangomuona, anayamba kung’amba zovala zake+ ndi kunena kuti: “Kalanga ine mwana wanga! Wandiweramitsa ndi chisoni ndipo ine ndikukupitikitsa. Ndatsegula pakamwa panga pamaso pa Yehova, ndipo sindingathe kubweza mawu anga.”+
26 Ngati munthu akudziona ngati wopembedza,+ koma salamulira lilime lake,+ ndipo akupitiriza kunyenga mtima wake,+ kupembedza kwa munthu ameneyu n’kopanda pake.+