Salimo 127:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 127 Yehova akapanda kumanga nyumba,+Omanga nyumbayo amagwira ntchito pachabe.+Yehova akapanda kulondera mzinda,+Alonda amakhala maso pachabe.+ Hagai 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndinalamula kuti chilala chigwe padziko lapansi, pamapiri, pambewu, pavinyo watsopano,+ pamafuta, pazinthu zonse zochokera munthaka, pa anthu, paziweto ndi pa ntchito iliyonse ya manja anu.’”+ 2 Yohane 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Samalani kuti musalephere kulandira mphoto ya zinthu zimene tazigwirira kale ntchito, kuti mudzalandire mphoto yokwanira.+
127 Yehova akapanda kumanga nyumba,+Omanga nyumbayo amagwira ntchito pachabe.+Yehova akapanda kulondera mzinda,+Alonda amakhala maso pachabe.+
11 Ndinalamula kuti chilala chigwe padziko lapansi, pamapiri, pambewu, pavinyo watsopano,+ pamafuta, pazinthu zonse zochokera munthaka, pa anthu, paziweto ndi pa ntchito iliyonse ya manja anu.’”+
8 Samalani kuti musalephere kulandira mphoto ya zinthu zimene tazigwirira kale ntchito, kuti mudzalandire mphoto yokwanira.+