Yesaya 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Vinyo watsopano akulira, ndipo mtengo wa mpesa wafota.+ Anthu onse amene anali kusangalala mumtima mwawo akuusa moyo.+ Hoseya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma iye sanavomereze+ kuti ndine amene ndinali kumupatsa mbewu,+ vinyo wotsekemera* ndi mafuta. Sanavomerezenso kuti ndine amene ndinamuchulukitsira siliva ndi golide amene iye anali kumugwiritsa ntchito popembedza Baala.+
7 Vinyo watsopano akulira, ndipo mtengo wa mpesa wafota.+ Anthu onse amene anali kusangalala mumtima mwawo akuusa moyo.+
8 Koma iye sanavomereze+ kuti ndine amene ndinali kumupatsa mbewu,+ vinyo wotsekemera* ndi mafuta. Sanavomerezenso kuti ndine amene ndinamuchulukitsira siliva ndi golide amene iye anali kumugwiritsa ntchito popembedza Baala.+