Yesaya 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kukondwera ndi kusangalala zachotsedwa m’munda wako wa zipatso, ndipo m’minda ya mpesa mulibe mfuu yachisangalalo. Mulibe aliyense amene akufuula.+ Mopondera mphesa mulibe amene akuponda vinyo.+ Ndachititsa kuti kufuula kulekeke.+ Yesaya 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Dzimenyeni pachifuwa pomva chisoni+ chifukwa cha kuwonongeka kwa minda yachonde+ ndi minda ya mpesa. Amosi 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ‘Padzakhala kulira mokweza m’minda yonse ya mpesa+ pakuti ine ndidzadutsa pakati panu,’+ watero Yehova.
10 Kukondwera ndi kusangalala zachotsedwa m’munda wako wa zipatso, ndipo m’minda ya mpesa mulibe mfuu yachisangalalo. Mulibe aliyense amene akufuula.+ Mopondera mphesa mulibe amene akuponda vinyo.+ Ndachititsa kuti kufuula kulekeke.+
12 Dzimenyeni pachifuwa pomva chisoni+ chifukwa cha kuwonongeka kwa minda yachonde+ ndi minda ya mpesa.
17 ‘Padzakhala kulira mokweza m’minda yonse ya mpesa+ pakuti ine ndidzadutsa pakati panu,’+ watero Yehova.