Yeremiya 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Pokolola ndidzawafafaniza,’ watero Yehova.+ ‘Mumtengo wa mpesa simudzapezeka mphesa,+ mumtengo wa mkuyu simudzapezeka nkhuyu, ndipo masamba adzafota. Zinthu zimene ndimawapatsa zidzawadutsa.’” Yoweli 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munda wawonongedwa+ ndipo nthaka ikulira+ pakuti mbewu zawonongedwa. Vinyo watsopano wauma+ ndipo mafuta atha.+
13 “‘Pokolola ndidzawafafaniza,’ watero Yehova.+ ‘Mumtengo wa mpesa simudzapezeka mphesa,+ mumtengo wa mkuyu simudzapezeka nkhuyu, ndipo masamba adzafota. Zinthu zimene ndimawapatsa zidzawadutsa.’”
10 Munda wawonongedwa+ ndipo nthaka ikulira+ pakuti mbewu zawonongedwa. Vinyo watsopano wauma+ ndipo mafuta atha.+