Yesaya 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Vinyo watsopano akulira, ndipo mtengo wa mpesa wafota.+ Anthu onse amene anali kusangalala mumtima mwawo akuusa moyo.+ Yoweli 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo achititsa mtengo wanga wa mpesa kukhala chinthu chodabwitsa+ ndipo mtengo wanga wa mkuyu ausandutsa chitsa.+ Nthambi za mitengo imeneyi azichotsa makungwa n’kuzitayira kutali.+ Mphukira zake azichotsa makungwa ndipo zauma.
7 Vinyo watsopano akulira, ndipo mtengo wa mpesa wafota.+ Anthu onse amene anali kusangalala mumtima mwawo akuusa moyo.+
7 Iwo achititsa mtengo wanga wa mpesa kukhala chinthu chodabwitsa+ ndipo mtengo wanga wa mkuyu ausandutsa chitsa.+ Nthambi za mitengo imeneyi azichotsa makungwa n’kuzitayira kutali.+ Mphukira zake azichotsa makungwa ndipo zauma.