Deuteronomo 28:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Udzalimadi ndi kubzala mitengo ya mpesa, koma sudzakolola mphesa zake ndi kumwa vinyo,+ chifukwa mbozi zidzadya mpesawo.+ Yesaya 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Vinyo watsopano akulira, ndipo mtengo wa mpesa wafota.+ Anthu onse amene anali kusangalala mumtima mwawo akuusa moyo.+ Hoseya 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Malo opunthira mbewu ndiponso oponderamo mphesa sakukupatsa chakudya,+ ndipo vinyo wotsekemera akukukhumudwitsa.+
39 Udzalimadi ndi kubzala mitengo ya mpesa, koma sudzakolola mphesa zake ndi kumwa vinyo,+ chifukwa mbozi zidzadya mpesawo.+
7 Vinyo watsopano akulira, ndipo mtengo wa mpesa wafota.+ Anthu onse amene anali kusangalala mumtima mwawo akuusa moyo.+
2 Malo opunthira mbewu ndiponso oponderamo mphesa sakukupatsa chakudya,+ ndipo vinyo wotsekemera akukukhumudwitsa.+