Hoseya 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Chotero ndidzatembenuka ndi kumulanda mbewu zanga pa nthawi yokolola. Ndidzalanda vinyo wanga wotsekemera pa nyengo yopanga vinyo.+ Ndidzamulandanso zovala zanga za ubweya wa nkhosa ndi nsalu zanga zimene amabisa nazo maliseche ake.+
9 “‘Chotero ndidzatembenuka ndi kumulanda mbewu zanga pa nthawi yokolola. Ndidzalanda vinyo wanga wotsekemera pa nyengo yopanga vinyo.+ Ndidzamulandanso zovala zanga za ubweya wa nkhosa ndi nsalu zanga zimene amabisa nazo maliseche ake.+