Yobu 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nthawi ya masana amakhala pakati pa migula ya m’minda.Amaponda mphesa koma amakhala ndi ludzu.+ Yoweli 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munda wawonongedwa+ ndipo nthaka ikulira+ pakuti mbewu zawonongedwa. Vinyo watsopano wauma+ ndipo mafuta atha.+
10 Munda wawonongedwa+ ndipo nthaka ikulira+ pakuti mbewu zawonongedwa. Vinyo watsopano wauma+ ndipo mafuta atha.+