Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Chotero pakati pa usiku, Yehova anapha mwana aliyense woyamba kubadwa m’dziko la Iguputo.+ Kuyambira mwana woyamba wa Farao, amene wakhala pampando wachifumu, mpaka mwana woyamba wa mkaidi amene ali m’ndende yapansi, ndiponso mwana woyamba kubadwa wa nyama iliyonse.+

  • Ekisodo 13:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma Farao anaumitsa mtima wake posalola kuti ife tichoke,+ motero Yehova anapha mwana woyamba kubadwa aliyense m’dziko la Iguputo,+ kuyambira mwana woyamba kubadwa wa munthu mpaka mwana woyamba kubadwa wa nyama.+ N’chifukwa chake tikupereka nsembe kwa Yehova ana onse a nyama oyamba kubadwa,+ ndipo tikuwombola mwana woyamba kubadwa aliyense mwa ana athu.’+

  • Salimo 105:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Mulungu anapha mwana aliyense woyamba kubadwa m’dziko lawo,+

      Chiyambi cha mphamvu zawo zonse zobereka.+

  • Salimo 135:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Wochita zimenezi ndiye anapha ana oyamba kubadwa a ku Iguputo,+

      Anapha ana a anthu ngakhalenso ana a nyama.+

  • Salimo 136:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Yamikani amene anakantha Aiguputo mwa kupha ana awo oyamba kubadwa:+

      Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena