Deuteronomo 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wachifundo.+ Sadzakutayani kapena kukuwonongani kapena kuiwala pangano+ la makolo anu limene anawalumbirira. Yoswa 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Palibe amene adzatha kulimbana nawe masiku onse a moyo wako.+ Ndidzakhala nawe+ monga mmene ndinakhalira ndi Mose, sindidzakutaya kapena kukusiya ngakhale pang’ono.+ Aheberi 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama,+ koma mukhale okhutira+ ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Pakuti Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pang’ono.”+
31 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wachifundo.+ Sadzakutayani kapena kukuwonongani kapena kuiwala pangano+ la makolo anu limene anawalumbirira.
5 Palibe amene adzatha kulimbana nawe masiku onse a moyo wako.+ Ndidzakhala nawe+ monga mmene ndinakhalira ndi Mose, sindidzakutaya kapena kukusiya ngakhale pang’ono.+
5 Moyo wanu ukhale wosakonda ndalama,+ koma mukhale okhutira+ ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Pakuti Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pang’ono.”+