Deuteronomo 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Limbani mtima ndipo chitani zinthu mwamphamvu.+ Musawaope kapena kuchita nawo mantha,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pang’ono.”+ 1 Mbiri 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zinthu zidzakuyendera bwino+ ukayesetsa kutsatira malamulo+ ndi zigamulo+ zimene Yehova analamula+ Mose zokhudza Isiraeli. Khala wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu.+ Usaope+ kapena kuchita mantha.+
6 Limbani mtima ndipo chitani zinthu mwamphamvu.+ Musawaope kapena kuchita nawo mantha,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pang’ono.”+
13 Zinthu zidzakuyendera bwino+ ukayesetsa kutsatira malamulo+ ndi zigamulo+ zimene Yehova analamula+ Mose zokhudza Isiraeli. Khala wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu.+ Usaope+ kapena kuchita mantha.+